Kofi mukudziwa amend adafa ndi Yesu

Kodi mukudziwa kuti amene adafa Ali ndi Yesu akuposa amene Ali ndi moyo koma opanda Yesu? Taganizani anthu amuna okhaokha kumagonana kapena akazi okhaokha, zomwe olo Galu sangachite.

Inu amene mulibe Yesu mukudziwa koma kuti Ambuye amakukondani? Si uyu muli pantchito yabwino,mudaphu

nzira,muli pabanja,ndinu olemera. Bwanji mulape lero posiya zigololo,mitala,ufiti,kuba,kuchotsa mimba,kuledzera,kusuta,kusintha amuna/akazi ngati sapato?

Ndikukuitanani ine m’bale wanu kuti bwerani kwa Yesu lero kuti mupulumuke. Mateyu 11:28-30.

Our pray this morning

 

OUR PRAYER THIS MORNING…

Oyera oyera oyera inu Tate wokhala kumwamba mwini chilengedwe..amene munalenga kumwamba ndi dziko lapansi kmanso ndi zonse zokhala momwemo..tikudza pamanso panu mogonja ndi moweramisa khope zathu pansi..kamba kachifundo ndi chikondi chomwe mwatiwonesera ife ana anu ochimwa..tikuti dzikomo potidzutsa ndi moyo chonchi..pomwe anzathu ena analephera kutero asikira kulichete…siife opambana ayi kma chifukwa chachikondi chanu..onan tsopano kwacha tikupephan mutiyang’anire tsiku lathu kut likhale lopambana..pali zambiri zomwe satana akhale akutitchera kma inu ambuye masulan misapha yonse kut isatenge gawo paife..

Akhuzen onse amene akuvutika ndi matenda..kmanso ayang’aniren abale omwe akuzuzika ndi nkhondo ndi uphawi..

Mu dzina loti Yesu christu tapempha izi..

# AMEN

 

 

 

 

There is people in your life

 

There people in your life who are eagerly

waiting to hear bad news about you that you

lost your job, your relationship or marriage

didn’t work out, you are jailed, you got an

accident that nearly took your life, you

completely gave up on your dreams, you lost

your property and loved ones or you acquired

an incurable disease.

.

But they are going to wait in vain. God is rather

going to Bless you and shame them. Just stay

focused and in faith