Anthu RNA anauyamba

 

Anthu ena anawuyamba opita ku jon kukasaka ntchito atakwela basi,nkulu wina anauyamba wapansi poti analibe transport.Akuyenda Azizake okwela basi anampeza pa malo ena,driver anamuvela chison nkuluyo atafunsa anthu mubasimo kuti mukumdziwa timtenge?

 

Anthu onse anakana chosecho amamumdziwa avekele ukamtenga zathu utibwezele.Anamdutsa nkuluyo mwamwai kumbuyo kumabwela galimoto ya zungu ndipo anamtenga nkuluyo.Basi inawonongeka anthu aja anakhala sabata pamsewu,nkulu uja atafika anamlemba ntchito ndipo anampatsa udindo oti azilemba ntchito anthu okhawo owaziwa.Anthu aja basi itakodzedwa anakafika bwino,koma anadabwa kuwona munthu yemwe amamukana kuti sakumdziwa ndi amene akulemba anthu ntchito.Atamfunsa anati pepeni sindikukuziwani

,anavutika kusowa ntchito apolis mpakana anawamanga kukawaika mundende.Mbale wangasamala Ambuye Yesu ananena kale kuti yense ondikana ine pamanso pa anthu nane ndikamkana pamanso pa atate wanga wa kumwamba,dziwa kuti ngati ukukana Yesu kumwamba sukalowa,mapeto ake akakuponya ku jahena.

 

Advertisements