Our pray this morning

 

OUR PRAYER THIS MORNING…

Oyera oyera oyera inu Tate wokhala kumwamba mwini chilengedwe..amene munalenga kumwamba ndi dziko lapansi kmanso ndi zonse zokhala momwemo..tikudza pamanso panu mogonja ndi moweramisa khope zathu pansi..kamba kachifundo ndi chikondi chomwe mwatiwonesera ife ana anu ochimwa..tikuti dzikomo potidzutsa ndi moyo chonchi..pomwe anzathu ena analephera kutero asikira kulichete…siife opambana ayi kma chifukwa chachikondi chanu..onan tsopano kwacha tikupephan mutiyang’anire tsiku lathu kut likhale lopambana..pali zambiri zomwe satana akhale akutitchera kma inu ambuye masulan misapha yonse kut isatenge gawo paife..

Akhuzen onse amene akuvutika ndi matenda..kmanso ayang’aniren abale omwe akuzuzika ndi nkhondo ndi uphawi..

Mu dzina loti Yesu christu tapempha izi..

# AMEN

 

 

 

 

Advertisements