Mateyu 7:26

 

Pa Mateyu 7:26,

Yesu akuti munthu amene amava mau a Mulungu koma asawagwiritsa ntchito Ali ngati munthu opusa amene amamanga nuyumba yake pa mchenga mvula ndi mphepo zikaiomba imagwa. Okondendwa mau a Mulungu akulalikidwa ndipo anthu akulemba ma comment akuti, Amen,go deeper, preach on! Koma mtakufusani mmachita zomwe mwavazo? Ngati ayi Yesu akuti muli ngati munthu opusa.

Ndikunena pano wina wakhala ukuwelenga mauthenga okuuza kuti ukuyenera kulapa ndi kukhulupilira Yesu kuti upulumuke koma umangoti Amen! Wakuva wamva uganiza bwanji umaona ngati zilibwino ukatero? Ukufanana ndi munthu opusa. Ndikunena pano tiri ndi ma president ambiri afanana andi anthu upusa,tiri ndi ma madotolo,a police, aziphuzitsi, ma MP, ma driver, nduna, oweruza milandu, oyimba, ana a school, ma bwana ndi ena ambiri amene amava mau a Mulungu koma osamawagwiritsa ntchito, Inu verani lero mukufanana ndi munthu opusa zilibe kunthu kuti ndinu olemekezeka,otchuka ndi amphamvu.

LAPANI LERO NDI KUYAMBA KUVA MAU A MULUNGU NDI KUWAGWIRITSANTSA NTCHITO KUTI MUKHALE OCHENJERANPA MASO PA MULUNGU

Amen

 

Advertisements