Bengo vs mkazi wake

Bengo vs mkazi wake

MKAZI: chifukwa chan mkundilesa kugwira fon yanu?

Bengo: muli zisisi zanga ndipo ukazagwira fon yanga uzawona chomwe chidameta nkhanga mpala,iwe yako ndimaigwira,dats y kubafa ndimanyamula fon yanga even kutoilet sindifuna munthu aliese aziwe zisisi zamufon mwanga!

Mkazi: ok ndilibe ulamuliro pot ndinu fumu ya banja!

Bengo: ukudziwa kale ubwino wake.

TSIKU LINA MKAZI ADASALA TULO,CHAMMA 1 KOLOKO USIKU PAMENE ADATENGA FON YABENGO,

Bengo nthawii adali mtulo,ndpo adapeza mameseji 10,

mesej yoyamba nayi: thanks for using pasavute mtolo,

yachwiri:u hav receivd 400bonus for TNM2TNM only,

yachtatu:u hav insuficient credit please recharge ur account,

ya#4: the #0882222 waz caling u 2hrs ago,

ya#5: mtolo 32 orderd succesfuly,

Ya#6: u hv receivd 32mtolo smss,

ya#7:eti alamu anu fon yawo yidawonongeka kma alibwino,

ya#8:akazi anu muwauze kt tasintha program yakuchurch ija,

ya#10:aixe akufuna mlonda kulima gold u can apply>>>>

mkazi adangoti kukamwa yasa uku akugwiragwira mmaso after kusala tulo inoder2see husbandz secrets

 

Advertisements