Bengo

 

Bengo……..hey sweet, ndili panja pa mpanda wakwanu

Girl……..iiiiiiih sorry ndatalikila ndili ku Lilongwe

Bengo…….eish ok ndinali ndi fifty thousand ndiye basi next time

Girl…….aaaaah chonde tangondipatsa 2 minutes ndikubwela

Bengo……..what? 2 minutes from Lilongwe to Blantyre zitheka bwanji?

Girl………ayiii ndili kwa a neba ndiye timangokutcha ku Lilongwe

Bengo…….oooooh ok…..ndiye pangatu changu bcoz ndili ndi mzanga uyu timamutcha fifty thousand watopa

Girl……..Zaugalu eti……..

kkkkkkkkkkk atambwali sametana samala ndi 2017 iyi

Advertisements