Bengo vs janet

14720343_1653442021614169_8386989480769454575_nBengo amacheza ndi chibwezi chake pa watsap…

 

 

 

Bengo:honey ndimafuna weekend ubwere kuden

 

Janet:sizithekacoz ndikuchokapo

 

Bengo:ukupita kutJanet:Ku ukwati wa mzanga

 

 

Bengo:ndiye mpaka kukanika kubwera,osajombako bwanji?

 

 

 

Janet:aaaa iwe sindingayelekeza…munthu oti taphunzila limodz,or patavuta sindingalepherekupitako tidzakumana weekend inayo

 

 

 

 

 

Bengo:ok bas coz ndimafuna tipite Ku nyanja tikasambe,malingana ndikutenthaku komanso ndimafuna nkakugulile zovala zija,koma ndiye basi apopo

 

 

Janet:basi ndibwera honey osadandaula ndimakukonda kwambir ndipo nzagona konko

 

 

 

 

Bengo:nanga ukwati wa mzakowo?Janet:ndimangonama honey

 

 

Bengo:inenso ndimangonama �…….moti pano chibwezi chatha

Advertisements