MOYO NDI WOWAWA KWA ACHRISTU ENI ENI PANO PADZIKO LAPANSI

images-3Moyo ndiwowawa kwa A Christ eni eni ziko lapansi ufulu palibe kwa Iwo popeza sife aziko lapansi ndife Alendo
#Luka 2:1-7 kubadwa kwa Yesu ,Marie ndi Yosefe anachoka kumuz kwao Nazareth ulendo ukalembesa kaundula Ku Bethlehem ,ndipo atafika uko nthande anapeza Marie kut abale ,anayenda chipatala chachikulu cha Bethlehem koma bible langa likut malo anasowa ,chipatala munazaza mpaka Yosefe anatenga kanz wake nachilila nkhola lang’ombe ,pulumutsi anabadwila nkhola la ng’ombe malo atasowa zipatala
kuteleko inali plan yasatana kupanga zotheka kut Yesu asabadwile malo awulemu.popeza soka tunda ndi nyanja oipayo wasikila kumeneko .satana aliphamvu yofuna kulephelesa plan ya Mulungu,Apa anthu kunali kuseka ,kunyoza Yesu kut inu zoona pulumusi mwana Wa Mulungu akabadwile nkhola la ng’ombe ,ndi picture imeneyo anthu ena sanakhulupilile iye,koma sizinalephelese kukhala mwana Wa Mulungu popeza anachita zozizwa zotse natifela ife pa tanda ,kukhala tembelelo malo mwanthu
Lelo linu anthu amakunyozan potengela dela ,chigawo ndinkhomo munabadwila kut ndinu olephela ,koma sinu olephela ngat muyima naye yesu uyu anabadwila malo onyozeka koma kuchita zazikulu
Malo anachepa,lelo lino kut mukafusile ntchito mungopeza anthu azazako kale atenga ena inu kubwelala malo mulibe,kotenga ngongole anthu amaliza malo anu kulibe,mukati muyambe business ena ayamba kale business maganizayo maloso atenga omwe mati mpange lent,apa mwasowa tengo ogwila nde Christ ameneyo zinthu zake zimakhala zoyendela chisomo ziko likukanisa malo
Sindikusamala kut mukudusa zotan Yesu sanasamale kut chipatala mwazaza anabadwila malo onyozeka,koma sizinasinthe plan ya Mulungu inuso pali mwai pena pake Wa ntchito yonyozeka lowan yomweyo,business yonyozeka yambani yomweyo Yesu akukwezan zomwezo ,ngat analemba muzakhala millions palibe chomulaka adusa muzonyozeka zomwezo mpaka anthu adabwa business yake iti ,ntchito yake iti mwatukuka nayo chochi kumangowawuza kuti ndili ndi Yesu wamayankho ,wazatheka bwanji

Advertisements